-
Chivumbulutso 18:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Zoonadi, chipatso chabwino chimene unkachilakalaka chija chakuchokera, ndipo zinthu zako zonse zabwino komanso zokongola zawonongeka ndipo anthu sadzazipezanso.
-