-
Chivumbulutso 18:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Amalonda amene ankagulitsa zinthu zimenezi, amene analemera chifukwa cha iye, adzaima patali chifukwa cha mantha poona mmene akuzunzikira ndipo adzamulirira ndi kumva chisoni.
-