16 Iwo azidzati: ‘Zomvetsa chisoni! Zomvetsa chisoni! Iwe mzinda waukulu, umene unkavala zovala zapamwamba, zapepo ndi zofiira kwambiri. Iwe mzinda umene unakongoletsedwa mochititsa chidwi ndi zodzikongoletsera zagolide, mwala wamtengo wapatali ndi ngale.+