Chivumbulutso 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sangalalani kumwambako chifukwa cha zimene zamuchitikira.+ Inunso oyera,+ atumwi ndi aneneri, sangalalani chifukwa Mulungu wamupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:20 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 268-269
20 Sangalalani kumwambako chifukwa cha zimene zamuchitikira.+ Inunso oyera,+ atumwi ndi aneneri, sangalalani chifukwa Mulungu wamupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+