-
Chivumbulutso 18:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kuimba kwa oimba pogwiritsa ntchito zeze, kwa oimba zitoliro, kwa oimba malipenga ndi kwa oimba ena sikudzamvekanso mwa iwe. Mwa iwe simudzapezekanso mmisiri wa ntchito iliyonse, komanso phokoso la mphero silidzamvekanso mwa iwe.
-