Chivumbulutso 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali+ lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Komanso iye ankapondaponda muchopondera mphesa cha mkwiyo waukulu wa Mulungu Wamphamvuyonse.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:15 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 282-284 Nsanja ya Olonda,5/15/1990, ptsa. 4-5
15 Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali+ lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Komanso iye ankapondaponda muchopondera mphesa cha mkwiyo waukulu wa Mulungu Wamphamvuyonse.+