Chivumbulutso 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mmodzi wa angelo 7 aja, amene anali ndi mbale 7 zodzaza ndi miliri 7 yotsiriza+ anabwera nʼkundiuza kuti: “Bwera kuno ndikuonetse mkwatibwi, mkazi wa Mwanawankhosa.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:9 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,2/15/2007, tsa. 13 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 305-306
9 Mmodzi wa angelo 7 aja, amene anali ndi mbale 7 zodzaza ndi miliri 7 yotsiriza+ anabwera nʼkundiuza kuti: “Bwera kuno ndikuonetse mkwatibwi, mkazi wa Mwanawankhosa.”+
21:9 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,2/15/2007, tsa. 13 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 305-306