Chivumbulutso 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anayezanso mpanda wake ndipo unali wautali mikono 144,* mogwirizana ndi muyezo umene munthu anapeza, umenenso ndi wofanana ndi muyezo wa mngelo. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:17 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 306-307
17 Anayezanso mpanda wake ndipo unali wautali mikono 144,* mogwirizana ndi muyezo umene munthu anapeza, umenenso ndi wofanana ndi muyezo wa mngelo.