-
Chivumbulutso 22:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Amene akuchita zosalungama, apitirize kuchita zosalungamazo ndipo amene akuchita zonyansa apitirizebe kuchita zonyansazo. Koma wolungama apitirize kuchita zachilungamo ndipo woyera apitirize kukhala woyera.
-