Genesis 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, Mulungu anauza Yakobo kuti: “Nyamuka, pita ku Beteli ukakhale kumeneko.+ Ukamangire guwa lansembe Mulungu woona, amene anaonekera kwa iwe pamene unali kuthawa Esau m’bale wako.”+
35 Zitatero, Mulungu anauza Yakobo kuti: “Nyamuka, pita ku Beteli ukakhale kumeneko.+ Ukamangire guwa lansembe Mulungu woona, amene anaonekera kwa iwe pamene unali kuthawa Esau m’bale wako.”+