Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Esau analinso kutchedwa Edomu.+