-
Genesis 36:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Potsiriza, nawa ana a Oholibama mkazi wa Esau: Mfumu Yeusi, mfumu Yalamu ndi mfumu Kora. Amenewa ndiwo anali mafumu a kubanja la Oholibama mkazi wa Esau, mwana wa Ana.
-