Genesis 36:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Bela atamwalira, Yobabi mwana wa Zera wa ku Bozira,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.+