Genesis 36:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yobabi atamwalira, Husamu wa kudziko la Atemani,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.+