Genesis 36:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Samila atamwalira, Shauli wa ku Rehoboti mzinda wa m’mphepete mwa Mtsinje,* anayamba kulamulira m’malo mwake.+
37 Samila atamwalira, Shauli wa ku Rehoboti mzinda wa m’mphepete mwa Mtsinje,* anayamba kulamulira m’malo mwake.+