-
Genesis 37:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ali pa ulendowo, munthu wina anakumana ndi Yosefe akungoyenda uku ndi uku kutchireko. Ndiyeno munthuyo anamufunsa kuti: “Kodi ukufunafuna chiyani?”
-