Genesis 37:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Amidiyani aja anakagulitsa Yosefe ku Iguputo kwa Potifara. Potifara anali nduna ya panyumba ya Farao,+ ndiponso anali mkulu wa asilikali olondera mfumu.+
36 Amidiyani aja anakagulitsa Yosefe ku Iguputo kwa Potifara. Potifara anali nduna ya panyumba ya Farao,+ ndiponso anali mkulu wa asilikali olondera mfumu.+