Genesis 41:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma zitadya zinzakezo, mimba za ng’ombe zowondazo sizinaoneke kuti mwalowa kanthu, popeza ng’ombezo zinaonekabe zowonda ngati poyamba.+ Pamenepo ndinagalamuka.
21 Koma zitadya zinzakezo, mimba za ng’ombe zowondazo sizinaoneke kuti mwalowa kanthu, popeza ng’ombezo zinaonekabe zowonda ngati poyamba.+ Pamenepo ndinagalamuka.