Genesis 41:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Njala ija inafalikira padziko lonse lapansi.+ Zitatero, Yosefe anayamba kutsegula nkhokwe zonse zimene zinali pakati pawo n’kuyamba kugulitsa chakudyacho kwa Aiguputo,+ chifukwa njalayo inali itakula kwambiri m’dziko la Iguputo.
56 Njala ija inafalikira padziko lonse lapansi.+ Zitatero, Yosefe anayamba kutsegula nkhokwe zonse zimene zinali pakati pawo n’kuyamba kugulitsa chakudyacho kwa Aiguputo,+ chifukwa njalayo inali itakula kwambiri m’dziko la Iguputo.