Genesis 43:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Isiraeliyo anadandaula+ kuti: “N’chifukwa chiyani munandipweteka chotero, pomuuza munthuyo kuti muli ndi m’bale wanu wina?”
6 Pamenepo Isiraeliyo anadandaula+ kuti: “N’chifukwa chiyani munandipweteka chotero, pomuuza munthuyo kuti muli ndi m’bale wanu wina?”