Genesis 43:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Potsirizira pake, Yuda anauza Isiraeli bambo ake kuti: “M’perekeni kwa ine mnyamatayu+ kuti tinyamuke tizipita. Tipite kuti tikhalebe ndi moyo tisafe,+ inuyo ndi ife, limodzi ndi ana athu aang’onowa.+
8 Potsirizira pake, Yuda anauza Isiraeli bambo ake kuti: “M’perekeni kwa ine mnyamatayu+ kuti tinyamuke tizipita. Tipite kuti tikhalebe ndi moyo tisafe,+ inuyo ndi ife, limodzi ndi ana athu aang’onowa.+