Genesis 43:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno amunawo anatenga mphatso zija, ndalama zowirikiza kawiri zija, ndiponso Benjamini, n’kunyamuka kupita ku Iguputo. Kumeneko anakaonekera pamaso pa Yosefe.+
15 Ndiyeno amunawo anatenga mphatso zija, ndalama zowirikiza kawiri zija, ndiponso Benjamini, n’kunyamuka kupita ku Iguputo. Kumeneko anakaonekera pamaso pa Yosefe.+