Genesis 43:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano munthuyo analowetsa amunawo m’nyumba ya Yosefe. Anawapatsa madzi kuti asambe mapazi awo,+ n’kuwapatsanso chakudya choti adyetse abulu awo.+
24 Tsopano munthuyo analowetsa amunawo m’nyumba ya Yosefe. Anawapatsa madzi kuti asambe mapazi awo,+ n’kuwapatsanso chakudya choti adyetse abulu awo.+