Genesis 47:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Yosefe anafikadi kwa Farao n’kumuuza kuti:+ “Bambo anga ndi abale anga abwera kuchokera ku Kanani. Abwera ndi nkhosa zawo, ng’ombe zawo ndi zonse zimene ali nazo, ndipo afikira ku Goseni.”+
47 Yosefe anafikadi kwa Farao n’kumuuza kuti:+ “Bambo anga ndi abale anga abwera kuchokera ku Kanani. Abwera ndi nkhosa zawo, ng’ombe zawo ndi zonse zimene ali nazo, ndipo afikira ku Goseni.”+