Genesis 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Yehova anati: “Ndidzaseseratu padziko lapansi anthu amene ndinawalenga.+ Kuyambira munthu, nyama yoweta, nyama yokwawa, mpaka cholengedwa chouluka m’mlengalenga,+ chifukwa ndikumva chisoni kuti ndinazipanga.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:7 Nsanja ya Olonda,4/15/1998, tsa. 7
7 Choncho Yehova anati: “Ndidzaseseratu padziko lapansi anthu amene ndinawalenga.+ Kuyambira munthu, nyama yoweta, nyama yokwawa, mpaka cholengedwa chouluka m’mlengalenga,+ chifukwa ndikumva chisoni kuti ndinazipanga.”+