Genesis 47:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa nthawi yokolola,+ muzipereka kwa Farao gawo limodzi mwa magawo asanu a zokololazo.+ Magawo anayi otsalawo muzigwiritsa ntchito monga mbewu yobzala m’minda yanu, chakudya chanu ndi cha a m’nyumba zanu, komanso cha ana anu.”+
24 Pa nthawi yokolola,+ muzipereka kwa Farao gawo limodzi mwa magawo asanu a zokololazo.+ Magawo anayi otsalawo muzigwiritsa ntchito monga mbewu yobzala m’minda yanu, chakudya chanu ndi cha a m’nyumba zanu, komanso cha ana anu.”+