Genesis 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma iweyo udzatenge chakudya cha mtundu uliwonse chodyedwa.+ Udzachisonkhanitse kuti chidzakhale chakudya chanu ndi cha zamoyo zinazo.”+
21 Koma iweyo udzatenge chakudya cha mtundu uliwonse chodyedwa.+ Udzachisonkhanitse kuti chidzakhale chakudya chanu ndi cha zamoyo zinazo.”+