Genesis 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo, Nowa anatuluka limodzi ndi ana ake,+ mkazi wake, ndi akazi a ana ake.