-
Genesis 2:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Panalinso mtsinje wochokera mu Edeni umene unali kuthirira mundawo. Potuluka mmenemo, mtsinjewo unayamba kugawikana n’kukhala mitsinje inayi.
-