Genesis 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano angelo awiri aja anafika ku Sodomu madzulo. Loti anali atakhala pachipata cha Sodomu.+ Atawaona ananyamuka kukakumana nawo, ndipo anawagwadira n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+
19 Tsopano angelo awiri aja anafika ku Sodomu madzulo. Loti anali atakhala pachipata cha Sodomu.+ Atawaona ananyamuka kukakumana nawo, ndipo anawagwadira n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+