Genesis 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Abulahamu anatenga mpeni uja kuti aphe mwana wakeyo.+