Genesis 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Abulahamu anaimirira n’kugwada pansi pamaso pa eni dzikowo,+ ana a Heti.+