Genesis 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ayi mbuyanga! Ndimvereni. Malowo, pamodzi ndi phanga limene lili pamalopo, ndikupatsani pamaso pa anthu a mtundu wangawa.+ Kaikeni malemuwo.”
11 “Ayi mbuyanga! Ndimvereni. Malowo, pamodzi ndi phanga limene lili pamalopo, ndikupatsani pamaso pa anthu a mtundu wangawa.+ Kaikeni malemuwo.”