Genesis 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero malo a Efuroni amene anali ku Makipela moyang’anizana ndi Mamure, ndiponso phanga limene linali mmenemo, komanso mitengo yonse imene inali mkati mwa malire onse a malowo,+ anatsimikizirika+
17 Chotero malo a Efuroni amene anali ku Makipela moyang’anizana ndi Mamure, ndiponso phanga limene linali mmenemo, komanso mitengo yonse imene inali mkati mwa malire onse a malowo,+ anatsimikizirika+