Genesis 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zitatero, Abulahamu anaika Sara mkazi wake m’manda kuphanga la Makipela, moyang’anizana ndi Mamure, kapena kuti Heburoni, m’dziko la Kanani.+
19 Zitatero, Abulahamu anaika Sara mkazi wake m’manda kuphanga la Makipela, moyang’anizana ndi Mamure, kapena kuti Heburoni, m’dziko la Kanani.+