Genesis 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikufuna ulumbire pali Yehova,+ Mulungu wakumwamba ndi Mulungu wa dziko lapansi, kuti sutengera mwana wanga mkazi pakati pa ana aakazi a Akanani, amene ndikukhala pakati pawo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:3 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2016, tsa. 14 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, ptsa. 25, 27
3 Ndikufuna ulumbire pali Yehova,+ Mulungu wakumwamba ndi Mulungu wa dziko lapansi, kuti sutengera mwana wanga mkazi pakati pa ana aakazi a Akanani, amene ndikukhala pakati pawo.+