Genesis 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma mtumikiyo anamufunsa kuti: “Bwanji ngati mkaziyo atakana kubwera nane kuno? Kodi ndidzatenge mwana wanuyu ndi kum’bwezera kudziko lanu kumene munachokera?”+
5 Koma mtumikiyo anamufunsa kuti: “Bwanji ngati mkaziyo atakana kubwera nane kuno? Kodi ndidzatenge mwana wanuyu ndi kum’bwezera kudziko lanu kumene munachokera?”+