Genesis 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ngati mkaziyo angakakane kubwera nawe, iweyo udzamasuka pa lumbiro limeneli.+ Koma zoti ukabwezere mwana wanga kumeneko, zimenezo ayi.”
8 Koma ngati mkaziyo angakakane kubwera nawe, iweyo udzamasuka pa lumbiro limeneli.+ Koma zoti ukabwezere mwana wanga kumeneko, zimenezo ayi.”