Genesis 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo mtumikiyo anatenga ngamila 10 pa ngamila za mbuye wake, n’kutenganso zabwino za mtundu uliwonse kwa mbuye wake zoti akazigwiritse ntchito.+ Kenako ananyamuka ulendo wopita ku Mesopotamiya, kumzinda wa Nahori. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:10 Nsanja ya Olonda,6/15/2011, ptsa. 16-177/1/1989, ptsa. 25, 27 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 6-7
10 Pamenepo mtumikiyo anatenga ngamila 10 pa ngamila za mbuye wake, n’kutenganso zabwino za mtundu uliwonse kwa mbuye wake zoti akazigwiritse ntchito.+ Kenako ananyamuka ulendo wopita ku Mesopotamiya, kumzinda wa Nahori.