Genesis 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno mtumikiyo anati: “Yehova, Mulungu wa mbuyanga Abulahamu,+ chonde chititsani kuti lero zinthu zindiyendere bwino, ndipo sonyezani mbuyanga Abulahamu kukoma mtima kwanu kosatha.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:12 Nsanja ya Olonda,3/1/2000, tsa. 3
12 Ndiyeno mtumikiyo anati: “Yehova, Mulungu wa mbuyanga Abulahamu,+ chonde chititsani kuti lero zinthu zindiyendere bwino, ndipo sonyezani mbuyanga Abulahamu kukoma mtima kwanu kosatha.+