Genesis 24:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ukakafika kwa abale anga, udzamasuka ku lumbiro limene wachita, ndiponso ngati sakakupatsa mkaziyo, udzamasuka ku lumbiroli.’+
41 Ukakafika kwa abale anga, udzamasuka ku lumbiro limene wachita, ndiponso ngati sakakupatsa mkaziyo, udzamasuka ku lumbiroli.’+