Genesis 24:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 ndaima pano pakasupe wa madzi. Zichitike kuti, namwali+ wotuluka mumzindawu kudzatunga madzi amene ndimuuze kuti, “Chonde, ndimweko pang’ono madzi a mumtsuko wakowo,”
43 ndaima pano pakasupe wa madzi. Zichitike kuti, namwali+ wotuluka mumzindawu kudzatunga madzi amene ndimuuze kuti, “Chonde, ndimweko pang’ono madzi a mumtsuko wakowo,”