Genesis 24:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Mtumiki wa Abulahamu atamva zimenezi, nthawi yomweyo anagwada n’kuweramira pansi pamaso pa Yehova.+
52 Mtumiki wa Abulahamu atamva zimenezi, nthawi yomweyo anagwada n’kuweramira pansi pamaso pa Yehova.+