Genesis 24:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Iye anawauza kuti: “Musandichedwetse, chifukwa Yehova wandithandiza kukwaniritsa zimene ndayendera.+ Ndiloleni ndizipita kwa mbuyanga.”+
56 Iye anawauza kuti: “Musandichedwetse, chifukwa Yehova wandithandiza kukwaniritsa zimene ndayendera.+ Ndiloleni ndizipita kwa mbuyanga.”+