Genesis 24:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Atatero, anafunsa mtumiki uja kuti: “Kodi munthu akubwera apoyo kuchokera m’tchire kudzakumana nafe ndani?” Mtumikiyo anayankha kuti: “Ameneyo ndi mbuyanga.” Pamenepo iye anatenga nsalu yophimba kumutu n’kudziphimba nayo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:65 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2016, tsa. 15
65 Atatero, anafunsa mtumiki uja kuti: “Kodi munthu akubwera apoyo kuchokera m’tchire kudzakumana nafe ndani?” Mtumikiyo anayankha kuti: “Ameneyo ndi mbuyanga.” Pamenepo iye anatenga nsalu yophimba kumutu n’kudziphimba nayo.+