-
Genesis 26:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Kenako iwo anakumbanso chitsime china, n’kukangananso za chitsimecho. Chitsimechi iye anachitcha Sitina.