Genesis 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atafika pamalo enaake anaona chitsime, ndipo panali magulu atatu a nkhosa zitagona pansi, chifukwa m’pamene anthu ankamwetsapo ziweto.+ Pachitsimepo+ panali potseka ndi mwala waukulu.
2 Atafika pamalo enaake anaona chitsime, ndipo panali magulu atatu a nkhosa zitagona pansi, chifukwa m’pamene anthu ankamwetsapo ziweto.+ Pachitsimepo+ panali potseka ndi mwala waukulu.