Genesis 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene Yakobo anali kuchokera kumunda madzulo,+ Leya anakamuchingamira n’kumuuza kuti: “Lero mugona ndi ine, chifukwa ine ndakugulani ndithu ndi mandereki a mwana wanga.” Usiku umenewo Yakobo anagonadi ndi Leya.+
16 Pamene Yakobo anali kuchokera kumunda madzulo,+ Leya anakamuchingamira n’kumuuza kuti: “Lero mugona ndi ine, chifukwa ine ndakugulani ndithu ndi mandereki a mwana wanga.” Usiku umenewo Yakobo anagonadi ndi Leya.+