Genesis 30:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Nthawi zonse ziweto zazikazi zamphamvu+ zikatentha thupi, Yakobo anali kuika timitengo tija m’ngalande momwera madzi+ kuti nkhosazo zitiyang’ane pamene zili zotentha thupi.
41 Nthawi zonse ziweto zazikazi zamphamvu+ zikatentha thupi, Yakobo anali kuika timitengo tija m’ngalande momwera madzi+ kuti nkhosazo zitiyang’ane pamene zili zotentha thupi.