Genesis 33:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chonde mbuyanga, tsogolani. Ine kapolo wanu ndizibwera m’mbuyo mwanu. Ndiziyenda pang’onopang’ono mogwirizana ndi mayendedwe a ziwetozi+ ndi kuyenda kwa anawa.+ Ndikakupezani ku Seiri, mbuyanga.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:14 Nsanja ya Olonda,11/1/2005, tsa. 18
14 Chonde mbuyanga, tsogolani. Ine kapolo wanu ndizibwera m’mbuyo mwanu. Ndiziyenda pang’onopang’ono mogwirizana ndi mayendedwe a ziwetozi+ ndi kuyenda kwa anawa.+ Ndikakupezani ku Seiri, mbuyanga.”+